2 Akorinto 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Katatu anandimenya ndi ndodo.+ Kamodzi anandiponya miyala.+ Ngalawa inandiswekerapo katatu.+ Kamodzi ndinakhala panyanja usiku ndi masana wonse. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:25 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, ptsa. 26-276/15/1990, ptsa. 12, 16
25 Katatu anandimenya ndi ndodo.+ Kamodzi anandiponya miyala.+ Ngalawa inandiswekerapo katatu.+ Kamodzi ndinakhala panyanja usiku ndi masana wonse.