2 Akorinto 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndinkagwira ntchito zowawa komanso zotulutsa thukuta. Nthawi zambiri usiku sindinkagona,+ ndinkakhala ndi njala ndiponso ludzu+ ndipo nthawi zambiri ndinkakhala osadya,+ ndinkazizidwa komanso ndinalibe zovala zokwanira.* 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:27 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, ptsa. 26-27
27 Ndinkagwira ntchito zowawa komanso zotulutsa thukuta. Nthawi zambiri usiku sindinkagona,+ ndinkakhala ndi njala ndiponso ludzu+ ndipo nthawi zambiri ndinkakhala osadya,+ ndinkazizidwa komanso ndinalibe zovala zokwanira.*