2 Akorinto 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikuyenera kudzitama. Choncho ndilankhula nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye,+ ngakhale kuti kudzitama kulibe phindu. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2018, tsa. 8
12 Ndikuyenera kudzitama. Choncho ndilankhula nkhani yokhudza masomphenya+ ndi mauthenga ochokera kwa Ambuye,+ ngakhale kuti kudzitama kulibe phindu.