-
2 Akorinto 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndikudziwa munthu wina wogwirizana ndi Khristu. Zaka 14 zapitazo, munthu ameneyu anatengedwa nʼkupita naye kumwamba kwachitatu. Kaya anatengedwa ali ndi thupi lake lenileni kapena ayi, sindikudziwa. Akudziwa ndi Mulungu.
-