-
2 Akorinto 12:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma ngakhale nditafuna kudzitama, sikuti ndikudzikweza, chifukwa ndikhala kuti ndikunena zoona. Koma sindichita zimenezo, popeza sindikufuna kuti wina anditamande kwambiri kuposa pa zinthu zimene akuona kapena kumva kwa ine,
-