9 Koma anandiuza kuti: “Kukoma mtima kwakukulu kumene ndakusonyeza nʼkokwanira, chifukwa mphamvu zanga zimaonekera bwino kwambiri iweyo ukakhala wofooka.”+ Choncho mosangalala kwambiri, ndidzadzitama pa zofooka zanga, kuti mphamvu za Khristu zikhalebe pamutu panga ngati tenti.