2 Akorinto 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndimasangalala ndi kufooka, kunyozedwa, kusowa zofunika pa moyo, kuzunzidwa ndiponso zovuta zina chifukwa cha Khristu. Chifukwa pamene ndili wofooka, mʼpamene ndimakhala wamphamvu.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2020, ptsa. 14-19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2018, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, tsa. 186/15/2008, ptsa. 3-4, 69/15/2004, ptsa. 13-14
10 Choncho ndimasangalala ndi kufooka, kunyozedwa, kusowa zofunika pa moyo, kuzunzidwa ndiponso zovuta zina chifukwa cha Khristu. Chifukwa pamene ndili wofooka, mʼpamene ndimakhala wamphamvu.+
12:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2020, ptsa. 14-19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2018, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, tsa. 186/15/2008, ptsa. 3-4, 69/15/2004, ptsa. 13-14