11 Tsopano ndakhala munthu wodzikweza. Koma ndi inuyo amene mwandikakamiza kuchita zimenezi, chifukwa munayenera kundiyamikira pa zabwino zimene ndachita. Ineyo sindikuchepa mwanjira ina iliyonse poyerekezera ndi atumwi anu apamwambawo, ngakhale kuti mumandiona ngati si ine kanthu.+