2 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi pali njira inanso yomwe tingati munali ndi mwayi wochepa kuyerekezera ndi mipingo yonse, kupatulapo kuti ineyo sindinakhale katundu wolemetsa kwa inu?+ Chonde ndikhululukireni tchimo limeneli lakuti sindinakhale katundu wolemetsa kwa inu.
13 Kodi pali njira inanso yomwe tingati munali ndi mwayi wochepa kuyerekezera ndi mipingo yonse, kupatulapo kuti ineyo sindinakhale katundu wolemetsa kwa inu?+ Chonde ndikhululukireni tchimo limeneli lakuti sindinakhale katundu wolemetsa kwa inu.