2 Akorinto 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndinalimbikitsa Tito kuti abwere kumeneko ndipo ndinamutumiza limodzi ndi mʼbale wina. Titoyo sanakudyereni masuku pamutu ngakhale pangʼono.+ Tinayenda mumzimu umodzi ndipo tinachita zinthu mofanana. Si choncho? 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:18 Nsanja ya Olonda,5/1/1988, ptsa. 16-17
18 Ndinalimbikitsa Tito kuti abwere kumeneko ndipo ndinamutumiza limodzi ndi mʼbale wina. Titoyo sanakudyereni masuku pamutu ngakhale pangʼono.+ Tinayenda mumzimu umodzi ndipo tinachita zinthu mofanana. Si choncho?