-
2 Akorinto 12:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kodi mwakhala mukuganiza kuti tikudziikira kumbuyo pamaso panu? Tikulankhula pamaso pa Mulungu mogwirizana ndi Khristu. Komatu okondedwa, tikuchita zonsezi kuti tikulimbikitseni.
-