2 Akorinto 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aka nʼkachitatu tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni* wochokera kwa mboni ziwiri kapena zitatu.”+
13 Aka nʼkachitatu tsopano kukonza ulendo wobwera kwanuko. “Muzitsimikizira nkhani iliyonse mutamva umboni* wochokera kwa mboni ziwiri kapena zitatu.”+