-
2 Akorinto 13:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ngakhale kuti sindili kumeneko zili ngati ndili nanu limodzi kachiwiri. Ndipo ndikuchenjezeratu anthu amene anachimwa komanso ena onse, kuti ndikangobweranso kumeneko sindidzawalekerera.
-