-
2 Akorinto 13:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsopano tikupemphera kwa Mulungu kuti musachite cholakwa chilichonse. Cholinga chathu si choti tioneke kuti ndife ovomerezeka, koma kuti inuyo muzichita zabwino, ngakhale ifeyo titaoneka ngati osavomerezeka.
-