-
Agalatiya 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiye kodi panopa ndikufuna kuti ndizikondedwa ndi anthu kapena Mulungu? Kapena kodi ndikungofuna kusangalatsa anthu? Ndikanakhala kuti ndikusangalatsabe anthu, sindikanakhala kapolo wa Khristu.
-