-
Agalatiya 1:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Uthengawu sindinaulandire kwa munthu ndipo sindinachite kuphunzitsidwa, koma Yesu Khristu ndi amene anandiululira uthenga umenewu.
-