Agalatiya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma kunena za anthu amene ankaoneka ngati apadera aja,+ kaya anali otani, zilibe kanthu kwa ine, chifukwa Mulungu sayangʼana maonekedwe a munthu, amuna odalirika amenewo sanandiphunzitse chilichonse chatsopano.
6 Koma kunena za anthu amene ankaoneka ngati apadera aja,+ kaya anali otani, zilibe kanthu kwa ine, chifukwa Mulungu sayangʼana maonekedwe a munthu, amuna odalirika amenewo sanandiphunzitse chilichonse chatsopano.