Agalatiya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 pajatu amene anapatsa Petulo mphamvu kuti akhale mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anandipatsanso ine mphamvu kuti ndikhale mtumwi kwa anthu a mitundu ina.+
8 pajatu amene anapatsa Petulo mphamvu kuti akhale mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anandipatsanso ine mphamvu kuti ndikhale mtumwi kwa anthu a mitundu ina.+