Agalatiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Kefa*+ atabwera ku Antiokeya,+ ndinamudzudzula* pamasomʼpamaso chifukwa zinali zoonekeratu kuti anachita zolakwika. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Nsanja ya Olonda,10/15/1989, tsa. 12
11 Koma Kefa*+ atabwera ku Antiokeya,+ ndinamudzudzula* pamasomʼpamaso chifukwa zinali zoonekeratu kuti anachita zolakwika.