-
Agalatiya 2:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndiye ngati ife tapezekanso kuti ndife ochimwa pamene tikuyesetsa kuti tiyesedwe olungama kudzera mwa Khristu, kodi ndiye kuti Khristu wakhala mtumiki wa uchimo? Ayi ndithu.
-