Agalatiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa choti ndinkatsatira chilamulo, ndinafa ku chilamulo+ kuti ndikhale moyo nʼkumatumikira Mulungu. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, tsa. 156/2021, tsa. 31
19 Chifukwa choti ndinkatsatira chilamulo, ndinafa ku chilamulo+ kuti ndikhale moyo nʼkumatumikira Mulungu.