Agalatiya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithudi mukudziwa kuti amene amakhalabe ndi chikhulupiriro ndi amene ali ana a Abulahamu.+