Agalatiya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kale malemba ananeneratu kuti Mulungu adzaona anthu a mitundu ina kuti ndi olungama chifukwa cha chikhulupiriro. Choncho analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu wakuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:8 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 86-87
8 Kale malemba ananeneratu kuti Mulungu adzaona anthu a mitundu ina kuti ndi olungama chifukwa cha chikhulupiriro. Choncho analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu wakuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+