Agalatiya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu ndi kwa mbadwa yake.*+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbadwa zako,”* ngati kuti mbadwazo nʼzambiri. Koma akunena kuti, “kwa mbadwa yako,”* kutanthauza kuti ndi imodzi, amene ndi Khristu.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2022, tsa. 16 Nsanja ya Olonda,2/1/1989, tsa. 12 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 117-118
16 Tsopano malonjezo anaperekedwa kwa Abulahamu ndi kwa mbadwa yake.*+ Malemba sanena kuti: “Kwa mbadwa zako,”* ngati kuti mbadwazo nʼzambiri. Koma akunena kuti, “kwa mbadwa yako,”* kutanthauza kuti ndi imodzi, amene ndi Khristu.+
3:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2022, tsa. 16 Nsanja ya Olonda,2/1/1989, tsa. 12 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 117-118