Agalatiya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa ngati Mulungu amapereka cholowa kudzera mʼchilamulo ndiye kuti sichidaliranso lonjezo. Koma mokoma mtima Mulungu wachipereka kwa Abulahamu kudzera mu lonjezo.+
18 Chifukwa ngati Mulungu amapereka cholowa kudzera mʼchilamulo ndiye kuti sichidaliranso lonjezo. Koma mokoma mtima Mulungu wachipereka kwa Abulahamu kudzera mu lonjezo.+