Agalatiya 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye nʼchifukwa chiyani Chilamulo chinaperekedwa? Anatipatsa Chilamulochi kuti machimo aonekere,+ mpaka mbadwa* imene inapatsidwa lonjezolo itafika.+ Angelo anapereka Chilamulocho+ kudzera mʼdzanja la mkhalapakati.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:19 Yandikirani, tsa. 193 Nsanja ya Olonda,2/1/1989, tsa. 13 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 75-80
19 Ndiye nʼchifukwa chiyani Chilamulo chinaperekedwa? Anatipatsa Chilamulochi kuti machimo aonekere,+ mpaka mbadwa* imene inapatsidwa lonjezolo itafika.+ Angelo anapereka Chilamulocho+ kudzera mʼdzanja la mkhalapakati.+
3:19 Yandikirani, tsa. 193 Nsanja ya Olonda,2/1/1989, tsa. 13 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 75-80