-
Agalatiya 3:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma Malemba amasonyeza kuti anthu akulamuliridwa ndi uchimo, kuti lonjezo limene limakhalapo chifukwa chokhulupirira Yesu Khristu, liperekedwe kwa anthu amene akumukhulupirira.
-