-
Agalatiya 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Tsopano ndikunena kuti, wolandira cholowa akakhala mwana wamngʼono, iye sasiyana ndi kapolo, ngakhale kuti ndi mwiniwake wa zinthu zonse.
-