Agalatiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nthawi itakwana, Mulungu anatumiza Mwana wake, amene anabadwa kudzera mwa mkazi+ ndipo anakhala pansi pa chilamulo.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Nsanja ya Olonda,9/15/1998, ptsa. 13-14
4 Koma nthawi itakwana, Mulungu anatumiza Mwana wake, amene anabadwa kudzera mwa mkazi+ ndipo anakhala pansi pa chilamulo.+