Agalatiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anachita zimenezi kuti apereke malipiro omasulira anthu amene anali pansi pa chilamulo+ nʼcholinga choti Mulungu atitenge nʼkukhala ana ake.+
5 Anachita zimenezi kuti apereke malipiro omasulira anthu amene anali pansi pa chilamulo+ nʼcholinga choti Mulungu atitenge nʼkukhala ana ake.+