Agalatiya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano popeza ndinu ana ake, Mulunguyo watumiza mzimu+ wa Mwana wake mʼmitima yathu+ ndipo mzimuwo ukufuula kuti: “Abba,* Atate!”+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,4/1/2009, tsa. 13
6 Tsopano popeza ndinu ana ake, Mulunguyo watumiza mzimu+ wa Mwana wake mʼmitima yathu+ ndipo mzimuwo ukufuula kuti: “Abba,* Atate!”+