Agalatiya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma panopa mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano mwadziwidwa ndi Mulungu. Ndiye mukubwereranso bwanji ku mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera, zomwe ndi zosathandiza+ ndiponso zopanda pake, nʼkumafuna kukhalanso akapolo ake?+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 8-9 Nsanja ya Olonda,3/15/2013, ptsa. 13-14
9 Koma panopa mwadziwa Mulungu, kapena tinene kuti tsopano mwadziwidwa ndi Mulungu. Ndiye mukubwereranso bwanji ku mfundo zimene anthu amʼdzikoli amayendera, zomwe ndi zosathandiza+ ndiponso zopanda pake, nʼkumafuna kukhalanso akapolo ake?+