Agalatiya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo ngakhale kuti matenda anga anali mayesero kwa inu, simunanyansidwe kapena kuipidwa nane.* Koma munandilandira ngati mngelo wa Mulungu kapena ngati Khristu Yesu. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:14 Galamukani!,6/8/1993, tsa. 16
14 Ndipo ngakhale kuti matenda anga anali mayesero kwa inu, simunanyansidwe kapena kuipidwa nane.* Koma munandilandira ngati mngelo wa Mulungu kapena ngati Khristu Yesu.