-
Agalatiya 4:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Anthu ena akuyesetsa kwambiri kuti akukopeni nʼcholinga choti muziwatsatira. Iwo sakuchita zimenezi ndi zolinga zabwino, koma akufuna kuti akuchotseni kwa ine, kuti inuyo muziwatsatira.
-