Agalatiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu ana anga,+ ndayambanso kumva kupweteka chifukwa cha inu ngati mayi amene watsala pangʼono kubereka. Ndipitiriza kumva kupweteka kumeneku mpaka mudzayambe kusonyeza makhalidwe a Khristu.
19 Inu ana anga,+ ndayambanso kumva kupweteka chifukwa cha inu ngati mayi amene watsala pangʼono kubereka. Ndipitiriza kumva kupweteka kumeneku mpaka mudzayambe kusonyeza makhalidwe a Khristu.