Agalatiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zinthu zimenezi zili ndi tanthauzo lophiphiritsira, chifukwa azimayi amenewa akuimira mapangano awiri. Loyamba ndi pangano la paphiri la Sinai,+ limene limabereka ana oti akhale akapolo. Pangano limenelo ndi Hagara uja. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:24 Nsanja ya Olonda,10/15/2014, tsa. 103/15/1992, tsa. 14 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 75-80
24 Zinthu zimenezi zili ndi tanthauzo lophiphiritsira, chifukwa azimayi amenewa akuimira mapangano awiri. Loyamba ndi pangano la paphiri la Sinai,+ limene limabereka ana oti akhale akapolo. Pangano limenelo ndi Hagara uja.
4:24 Nsanja ya Olonda,10/15/2014, tsa. 103/15/1992, tsa. 14 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 75-80