Agalatiya 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri lomwe lili ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, chifukwa ali mu ukapolo pamodzi ndi ana ake. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:25 Nsanja ya Olonda,3/15/1992, ptsa. 14-15
25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri lomwe lili ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, chifukwa ali mu ukapolo pamodzi ndi ana ake.