Agalatiya 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa Malemba amati: “Sangalala, mkazi wosabereka iwe amene sunaberekepo mwana. Fuula mosangalala, iwe mkazi amene sunamvepo zowawa za pobereka, chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiri kuposa ana a mkazi amene ali ndi mwamuna.”+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:27 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 118/1/1995, tsa. 11
27 Chifukwa Malemba amati: “Sangalala, mkazi wosabereka iwe amene sunaberekepo mwana. Fuula mosangalala, iwe mkazi amene sunamvepo zowawa za pobereka, chifukwa ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiri kuposa ana a mkazi amene ali ndi mwamuna.”+