Agalatiya 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mofanana ndi mmene zinalili pa nthawiyo, kuti amene anabadwa ngati mmene ana onse amabadwira anayamba kuzunza amene anabadwa kudzera mwa mzimu,+ ndi mmenenso zilili masiku ano.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:29 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, ptsa. 11-128/15/2001, tsa. 267/1/1989, tsa. 21
29 Koma mofanana ndi mmene zinalili pa nthawiyo, kuti amene anabadwa ngati mmene ana onse amabadwira anayamba kuzunza amene anabadwa kudzera mwa mzimu,+ ndi mmenenso zilili masiku ano.+