Agalatiya 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kunena za ine abale, ngati ndikulalikirabe kuti anthu azidulidwa, nʼchifukwa chiyani ndikuzunzidwabe? Zikanakhala choncho, ndiye kuti zimene ndimaphunzitsa zokhudza imfa ya Yesu pamtengo wozunzikirapo,*+ sizikanakhumudwitsanso anthu.
11 Kunena za ine abale, ngati ndikulalikirabe kuti anthu azidulidwa, nʼchifukwa chiyani ndikuzunzidwabe? Zikanakhala choncho, ndiye kuti zimene ndimaphunzitsa zokhudza imfa ya Yesu pamtengo wozunzikirapo,*+ sizikanakhumudwitsanso anthu.