Agalatiya 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onse amene akufuna kuti azioneka ngati abwino pamaso pa anthu ndi amene akukuumirizani kuti mudulidwe. Iwo akuchita zimenezi kuti asazunzidwe chifukwa cha mtengo wozunzikirapo* wa Khristu. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda,2/15/1989, ptsa. 19-20
12 Onse amene akufuna kuti azioneka ngati abwino pamaso pa anthu ndi amene akukuumirizani kuti mudulidwe. Iwo akuchita zimenezi kuti asazunzidwe chifukwa cha mtengo wozunzikirapo* wa Khristu.