Agalatiya 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma onse amene amatsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu,+ akhale ndi mtendere ndipo Mulungu awasonyeze chifundo. Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:16 Nsanja ya Olonda,7/1/1995, ptsa. 11-123/15/1987, ptsa. 15-16 Kukambitsirana, tsa. 46
16 Koma onse amene amatsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu,+ akhale ndi mtendere ndipo Mulungu awasonyeze chifundo.