Aefeso 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, ndine mtumwi wa Khristu Yesu ndipo ndikulembera oyera amene ali ku Efeso,+ amene ndi ophunzira a Khristu Yesu okhulupirika kuti:
1 Ine Paulo, mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, ndine mtumwi wa Khristu Yesu ndipo ndikulembera oyera amene ali ku Efeso,+ amene ndi ophunzira a Khristu Yesu okhulupirika kuti: