14 Mzimu woyerawo uli ngati chikole chotsimikizira kuti tidzalandira zimene Mulungu watilonjeza.+ Mulungu anachita zimenezi nʼcholinga choti apereke dipo+ kuti anthu ake amasulidwe.+ Zimenezi zidzachititsa kuti atamandidwe komanso kupatsidwa ulemerero.