Aefeso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru kuti mumvetse zimene Iye akuulula pamene mukuphunzira kuti mumudziwe molondola.+
17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru kuti mumvetse zimene Iye akuulula pamene mukuphunzira kuti mumudziwe molondola.+