Aefeso 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anamuika pamwamba kuposa boma lililonse, ulamuliro uliwonse, anthu amphamvu onse, ambuye onse, ndi aliyense amene ali ndi dzina laulemu,+ osati mu nthawi* ino yokha, komanso imene ikubwerayo.
21 Anamuika pamwamba kuposa boma lililonse, ulamuliro uliwonse, anthu amphamvu onse, ambuye onse, ndi aliyense amene ali ndi dzina laulemu,+ osati mu nthawi* ino yokha, komanso imene ikubwerayo.