Aefeso 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anachita zimenezi kuti mu nthawi* zimene zikubwera, iye adzatisonyeze chuma chopambana cha kukoma mtima kwake kwakukulu. Mulungu adzachita zimenezi potisonyeza chifundo chifukwa ndife ophunzira a Khristu Yesu. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, tsa. 29
7 Anachita zimenezi kuti mu nthawi* zimene zikubwera, iye adzatisonyeze chuma chopambana cha kukoma mtima kwake kwakukulu. Mulungu adzachita zimenezi potisonyeza chifundo chifukwa ndife ophunzira a Khristu Yesu.