-
Aefeso 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma tsopano mogwirizana ndi Khristu Yesu, inu amene pa nthawi ina munali kutali, mwabwera pafupi chifukwa cha magazi a Khristu.
-