Aefeso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo,*+ agwirizanitse magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu ndipo anthuwo akhale thupi limodzi, chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mu imfa yake.
16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo,*+ agwirizanitse magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu ndipo anthuwo akhale thupi limodzi, chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mu imfa yake.