6 Chinsinsi chimenechi nʼchakuti anthu a mitundu ina amene ndi ogwirizana ndi Khristu Yesu, adzalandire cholowa chimene Khristu adzalandire, ndipo adzakhala mbali ya thupi.+ Iwo adzalandiranso zinthu zimene Mulungu watilonjeza chifukwa cha uthenga wabwino.